2 Samueli 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ulamuliro wake umakhala ngati kuwala kwa m’mawa pamene dzuwa lawala,+M’mawa wopanda mitambo.Umakhala ngati msipu womera padziko mvula ikakata, dzuwa n’kuwala.’+
4 Ulamuliro wake umakhala ngati kuwala kwa m’mawa pamene dzuwa lawala,+M’mawa wopanda mitambo.Umakhala ngati msipu womera padziko mvula ikakata, dzuwa n’kuwala.’+