Ekisodo 33:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yehova anali kulankhula ndi Mose pamasom’pamaso,+ mmene munthu amalankhulira ndi munthu mnzake. Mose akabwerera kumsasa, mtumiki wake+ Yoswa, mwana wa Nuni,+ sanali kuchoka m’chihemacho, popeza anali kalinde. Ekisodo 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo anawonjezera kuti: “Sungathe kuona nkhope yanga, chifukwa palibe munthu angandione n’kukhalabe ndi moyo.”+ Numeri 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimalankhula naye pamasom’pamaso,+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa,+ ndipo amaona maonekedwe a Yehova.+ Tsopano n’chifukwa chiyani inu simunaope kum’nena Mose mtumiki wanga?”+
11 Pamenepo Yehova anali kulankhula ndi Mose pamasom’pamaso,+ mmene munthu amalankhulira ndi munthu mnzake. Mose akabwerera kumsasa, mtumiki wake+ Yoswa, mwana wa Nuni,+ sanali kuchoka m’chihemacho, popeza anali kalinde.
20 Ndipo anawonjezera kuti: “Sungathe kuona nkhope yanga, chifukwa palibe munthu angandione n’kukhalabe ndi moyo.”+
8 Ndimalankhula naye pamasom’pamaso,+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa,+ ndipo amaona maonekedwe a Yehova.+ Tsopano n’chifukwa chiyani inu simunaope kum’nena Mose mtumiki wanga?”+