Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Muzichita mosamala mawu onse amene ndikukuuzani.+ Musawonjezepo kapena kuchotsapo kalikonse.+

  • Yoswa 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Iwe khala wolimba mtima kwambiri ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Uonetsetse kuti ukutsatira malamulo onse amene mtumiki wanga Mose anakulamula.+ Malamulowo usawasiye ndi kupatukira kudzanja lamanja kapena lamanzere,+ kuti uchite mwanzeru kulikonse kumene udzapitako.+

  • Miyambo 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Usawonjezere kanthu pa mawu ake+ kuti angakudzudzule ndiponso kuti ungakhale wabodza.+

  • Chivumbulutso 22:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Ine ndikuchitira umboni kwa aliyense wakumva mawu a ulosi wa mumpukutuwu, kuti: Wina akawonjezera+ pa zimenezi, Mulungu adzamuwonjezera miliri+ yolembedwa mumpukutuwu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena