1 Timoteyo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akhale mwamuna woyang’anira bwino banja lake+ ndiponso akhale woti ana ake amamumvera ndi mtima wonse.+ 1 Timoteyo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Asakhale wotembenuka kumene,+ kuopera kuti angakhale wotukumuka chifukwa cha kunyada,+ n’kulandira chiweruzo chofanana ndi chimene Mdyerekezi analandira.+
4 Akhale mwamuna woyang’anira bwino banja lake+ ndiponso akhale woti ana ake amamumvera ndi mtima wonse.+
6 Asakhale wotembenuka kumene,+ kuopera kuti angakhale wotukumuka chifukwa cha kunyada,+ n’kulandira chiweruzo chofanana ndi chimene Mdyerekezi analandira.+