Ekisodo 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo anthuwo anauza Mose kuti: “Iweyo uzilankhula ndi ife, ndipo ife tizimvetsera, koma Mulungu asalankhule ndi ife kuopera kuti tingafe.”+ Aheberi 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Simunafike paphiri limene panamveka kulira kwa lipenga+ ndi mawu a winawake akulankhula,+ amene anthu atawamva, anachonderera kuti asawauzenso mawu ena.+
19 Ndipo anthuwo anauza Mose kuti: “Iweyo uzilankhula ndi ife, ndipo ife tizimvetsera, koma Mulungu asalankhule ndi ife kuopera kuti tingafe.”+
19 Simunafike paphiri limene panamveka kulira kwa lipenga+ ndi mawu a winawake akulankhula,+ amene anthu atawamva, anachonderera kuti asawauzenso mawu ena.+