Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Choncho uwauze ana a Isiraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova. Ndithu, ndidzakutulutsani mu Iguputo ndi kukuchotserani goli lawo, ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wawo.+ Ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasula komanso ndi ziweruzo zamphamvu.+

  • Ekisodo 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chotero Mose anauza anthuwo kuti: “Muzikumbukira tsiku lino limene munatuluka mu Iguputo,+ m’nyumba ya ukapolo, chifukwa Yehova anakutulutsani mmenemo ndi mphamvu ya dzanja lake.+ Choncho musadye chilichonse chokhala ndi chofufumitsa.+

  • Yesaya 51:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unasandutsa pansi pa nyanja kukhala njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena