Deuteronomo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inuyo mukudziwa bwino lero, (sindikulankhulatu ndi ana anu amene sanadziwe ndi kuona chilango* cha Yehova+ Mulungu wanu, ukulu wake+ ndi dzanja lake lamphamvu+ ndi mkono wake wotambasula,+
2 Inuyo mukudziwa bwino lero, (sindikulankhulatu ndi ana anu amene sanadziwe ndi kuona chilango* cha Yehova+ Mulungu wanu, ukulu wake+ ndi dzanja lake lamphamvu+ ndi mkono wake wotambasula,+