Deuteronomo 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 yokhalanso ndi nyumba zodzaza ndi zinthu zonse zabwino zimene sunaikemo ndiwe, ndi zitsime* zimene sunakumbe ndiwe, minda ya mpesa ndi mitengo ya maolivi imene sunabzale ndiwe, n’kudya ndi kukhuta,+ Deuteronomo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Mukadzadya ndi kukhuta+ mudzatamandenso+ Yehova Mulungu wanu, chifukwa cha dziko labwino limene wakupatsani.+ Yoweli 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo Yehova adzayankha ndi kuuza anthu ake kuti, ‘Tsopano ndikukutumizirani mbewu, vinyo watsopano ndi mafuta. Anthu inu mudzakhutadi zinthu zimenezi.+ Ine sindidzakuchititsaninso kukhala chinthu chotonzedwa pakati pa anthu a mitundu ina.+
11 yokhalanso ndi nyumba zodzaza ndi zinthu zonse zabwino zimene sunaikemo ndiwe, ndi zitsime* zimene sunakumbe ndiwe, minda ya mpesa ndi mitengo ya maolivi imene sunabzale ndiwe, n’kudya ndi kukhuta,+
10 “Mukadzadya ndi kukhuta+ mudzatamandenso+ Yehova Mulungu wanu, chifukwa cha dziko labwino limene wakupatsani.+
19 Pamenepo Yehova adzayankha ndi kuuza anthu ake kuti, ‘Tsopano ndikukutumizirani mbewu, vinyo watsopano ndi mafuta. Anthu inu mudzakhutadi zinthu zimenezi.+ Ine sindidzakuchititsaninso kukhala chinthu chotonzedwa pakati pa anthu a mitundu ina.+