Yoswa 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Malo alionse amene phazi lanu lidzapondapo ndidzawapereka ndithu kwa inu, monga mmene ndinalonjezera kwa Mose.+ Yoswa 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero Mose anandilumbirira tsiku limenelo kuti, ‘Dziko limene wakaliponda ndi mapazi ako+ lidzakhala cholowa chako ndi cha ana ako mpaka kalekale, chifukwa watsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wako wonse.’+
3 Malo alionse amene phazi lanu lidzapondapo ndidzawapereka ndithu kwa inu, monga mmene ndinalonjezera kwa Mose.+
9 Chotero Mose anandilumbirira tsiku limenelo kuti, ‘Dziko limene wakaliponda ndi mapazi ako+ lidzakhala cholowa chako ndi cha ana ako mpaka kalekale, chifukwa watsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wako wonse.’+