Deuteronomo 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita monga mmene Yehova Mulungu wanu wakulamulirani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Deuteronomo 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Muzichita mosamala mawu onse amene ndikukuuzani.+ Musawonjezepo kapena kuchotsapo kalikonse.+ Salimo 119:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mwatilamula kuti tisunge+Malamulo anu mosamala.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
32 Ndipo anthu inu muonetsetse kuti mukuchita monga mmene Yehova Mulungu wanu wakulamulirani.+ Musatembenukire kudzanja lamanja kapena lamanzere.+
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+