Levitiko 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “‘Munthu akakhudza chinthu chodetsedwa, kaya ikhale nyama yakufa yakuthengo, nyama yakufa yoweta, kapena kamodzi mwa tizilombo topezeka tambiri,+ ngakhale kuti sanazindikire zotsatira zake,+ iye ndi wodetsedwa ndipo wapalamula mlandu.+ Levitiko 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno wansembeyo aone nthenda imene yatuluka pakhunguyo.+ Ngati cheya cha pamalopo chasanduka choyera ndipo pakuoneka kuti m’pozama kupitirira khungu, ndiye kuti limenelo ndi khate. Wansembe aone nthendayo n’kugamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa.
2 “‘Munthu akakhudza chinthu chodetsedwa, kaya ikhale nyama yakufa yakuthengo, nyama yakufa yoweta, kapena kamodzi mwa tizilombo topezeka tambiri,+ ngakhale kuti sanazindikire zotsatira zake,+ iye ndi wodetsedwa ndipo wapalamula mlandu.+
3 Ndiyeno wansembeyo aone nthenda imene yatuluka pakhunguyo.+ Ngati cheya cha pamalopo chasanduka choyera ndipo pakuoneka kuti m’pozama kupitirira khungu, ndiye kuti limenelo ndi khate. Wansembe aone nthendayo n’kugamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa.