Deuteronomo 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Ndiyeno Yehova Mulungu wako akadzakulowetsa m’dziko limene analumbirira makolo ako Abulahamu, Isaki ndi Yakobo kuti adzakupatsa,+ dziko lokhala ndi mizinda ikuluikulu yooneka bwino imene sunamange ndiwe,+ Salimo 105:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pang’onopang’ono anawapatsa mayiko a anthu a mitundu ina,+Ndipo zipatso za ntchito imene mitundu ya anthu inagwira mwakhama, anazitenga kukhala zawo,+
10 “Ndiyeno Yehova Mulungu wako akadzakulowetsa m’dziko limene analumbirira makolo ako Abulahamu, Isaki ndi Yakobo kuti adzakupatsa,+ dziko lokhala ndi mizinda ikuluikulu yooneka bwino imene sunamange ndiwe,+
44 Pang’onopang’ono anawapatsa mayiko a anthu a mitundu ina,+Ndipo zipatso za ntchito imene mitundu ya anthu inagwira mwakhama, anazitenga kukhala zawo,+