Yeremiya 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ndamva zimene aneneri akulosera monama m’dzina langa+ kuti, ‘Ndalota maloto! Ndalota maloto!’+ Yeremiya 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘“‘Anthu inu musamvere aneneri,+ ochita zamaula, olota maloto,+ ochita zamatsenga ndi obwebweta+ amene ali pakati panu ndipo akukuuzani kuti: “Anthu inu simudzatumikira mfumu ya Babulo.”+
9 “‘“‘Anthu inu musamvere aneneri,+ ochita zamaula, olota maloto,+ ochita zamatsenga ndi obwebweta+ amene ali pakati panu ndipo akukuuzani kuti: “Anthu inu simudzatumikira mfumu ya Babulo.”+