11 Kenako Hananiya+ anauza anthu onse amene anali pamenepo kuti: “Yehova wanena kuti,+ ‘Pa zaka ziwiri zokha, ndithyola goli la Nebukadinezara mfumu ya Babulo limene waveka mitundu yonse ya anthu monga mmene ndathyolera goli ili.’”+ Zitatero, Yeremiya anachokapo.+