Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 13:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mneneri wokalambayo atamva zimenezi, anati: “Inenso ndine mneneri ngati iweyo. Mngelo+ wandiuza mawu ochokera kwa Yehova akuti, ‘Kam’bweze upite naye kunyumba kwako kuti akadye chakudya ndi kumwa madzi.’” (Anamunamiza.)+

  • 2 Mbiri 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Zedekiya mwana wa Kenaana anapanga nyanga+ zachitsulo n’kunena kuti: “Yehova wanena kuti,+ ‘Ndi nyanga izi mudzakankha Asiriya mpaka kuwatha.’”+

  • Yeremiya 23:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Anthu inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense woumitsa mtima wake+ akumuuza kuti, ‘Tsoka silidzakugwerani anthu inu.’+

  • Yeremiya 29:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pakuti ‘zimene akukuuzanizo akulosera m’dzina langa monama. Ine sindinawatume,’+ watero Yehova.”’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena