Numeri 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Munthu ameneyo wanyoza mawu a Yehova,+ ndipo waphwanya malamulo ake.+ Aziphedwa ndithu mosalephera.+ Mlandu wa cholakwa chake uzikhala ndi iye mwini.’”+ Deuteronomo 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha, ndipo sadzachita chinthu choipa chilichonse chofanana ndi chimenechi pakati panu.+ Deuteronomo 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero ena onse adzamva ndi kuchita mantha, ndipo sadzachitanso choipa chilichonse ngati chimenechi pakati panu.+
31 Munthu ameneyo wanyoza mawu a Yehova,+ ndipo waphwanya malamulo ake.+ Aziphedwa ndithu mosalephera.+ Mlandu wa cholakwa chake uzikhala ndi iye mwini.’”+
11 Pamenepo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha, ndipo sadzachita chinthu choipa chilichonse chofanana ndi chimenechi pakati panu.+
20 Chotero ena onse adzamva ndi kuchita mantha, ndipo sadzachitanso choipa chilichonse ngati chimenechi pakati panu.+