Deuteronomo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu onse adzamva zimenezo ndi kuchita mantha+ ndipo sadzadzikuzanso. Deuteronomo 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero ena onse adzamva ndi kuchita mantha, ndipo sadzachitanso choipa chilichonse ngati chimenechi pakati panu.+ 1 Timoteyo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ena mwa amenewa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda,+ ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa,* aphunzire kuti sayenera kulankhula zonyoza Mulungu.+ 1 Timoteyo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uwadzudzule+ pamaso pa onse kuti ena onse akhale ndi mantha.+
20 Chotero ena onse adzamva ndi kuchita mantha, ndipo sadzachitanso choipa chilichonse ngati chimenechi pakati panu.+
20 Ena mwa amenewa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda,+ ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa,* aphunzire kuti sayenera kulankhula zonyoza Mulungu.+
20 Anthu amene ali ndi chizolowezi chochita tchimo,+ uwadzudzule+ pamaso pa onse kuti ena onse akhale ndi mantha.+