Deuteronomo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 koma mudzafunefune malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe pakati pa mafuko anu onse kuti aikepo dzina lake, kuti lizikhala pamenepo. Amenewo ndiwo malo amene muzidzapitako.+ Deuteronomo 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Uzipereka nsembe ya pasika kwa Yehova Mulungu wako.+ Uzipereka nkhosa ndi ng’ombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Salimo 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova, ine ndimakonda nyumba imene inu mumakhala+Ndi malo amene kumakhala ulemerero wanu.+
5 koma mudzafunefune malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe pakati pa mafuko anu onse kuti aikepo dzina lake, kuti lizikhala pamenepo. Amenewo ndiwo malo amene muzidzapitako.+
2 Uzipereka nsembe ya pasika kwa Yehova Mulungu wako.+ Uzipereka nkhosa ndi ng’ombe+ pamalo amene Yehova adzasankhe kuikapo dzina lake.+