43 Mizinda yake ndi Bezeri,+ m’chipululu cha dera lokwererapo, wothawirako Arubeni, mzinda wa Ramoti+ ku Giliyadi, wothawirako Agadi, ndi mzinda wa Golani+ ku Basana, wothawirako Amanase.+
27 Ana a Gerisoni+ a m’mabanja a Alevi, anapatsidwa mizinda kuchokera ku hafu ya fuko la Manase.+ Anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake, wa Golani+ ku Basana, ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Beesitera+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Inalipo mizinda iwiri.
71 Kuchokera ku banja la hafu ya fuko la Manase, anapatsa ana a Gerisomu+ mzinda wa Golani+ ku Basana ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Asitaroti+ ndi malo ake odyetserako ziweto.