Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 46:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ana a Levi+ anali Gerisoni,+ Kohati+ ndi Merari.+

  • Numeri 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mwa ana a Kohati, panali banja la Aamuramu, banja la Aizara, banja la Aheburoni ndi banja la Auziyeli. Awa ndiwo anali mabanja a Akohati.+

  • Numeri 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Amuna onse owerengedwa, kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo, analipo 8,600. Ntchito ya amenewa inali kutumikira pamalo oyera.+

  • Numeri 3:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ntchito yawo+ inali yosamalira likasa,+ tebulo,+ choikapo nyale,+ maguwa ansembe,+ ndi ziwiya+ za m’malo oyerawo zimene anali kutumikira nazo, ndiponso nsalu yotchinga,+ komanso ntchito zonse zokhudza utumikiwu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena