Yoswa 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maere+ oyamba anagwera fuko la ana a Benjamini+ potsata mabanja awo, ndipo gawo limene anapatsidwa linali pakati pa ana a Yuda+ ndi ana a Yosefe.+ 1 Mbiri 6:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Kuchokera ku fuko la Benjamini, anawapatsa mzinda wa Geba+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Alemeti+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Anatoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Mizinda yonse ya mabanja awo inalipo 13.+
11 Maere+ oyamba anagwera fuko la ana a Benjamini+ potsata mabanja awo, ndipo gawo limene anapatsidwa linali pakati pa ana a Yuda+ ndi ana a Yosefe.+
60 Kuchokera ku fuko la Benjamini, anawapatsa mzinda wa Geba+ ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Alemeti+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso mzinda wa Anatoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Mizinda yonse ya mabanja awo inalipo 13.+