Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 2:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kwa wansembe Abiyatara,+ mfumuyo inati: “Pita kuminda yako ku Anatoti+ chifukwa ukuyenera kufa.+ Koma lero sindikupha, poti unanyamula likasa la Yehova Ambuye Wamkulu Koposa+ pamaso pa Davide bambo anga,+ ndiponso chifukwa chakuti unavutika nthawi yonse imene bambo anga anavutika.”+

  • Yesaya 10:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Iwe mwana wamkazi wa Galimu,+ fuula kwambiri. Khala tcheru, iwe Laisa. Iwenso Anatoti wosautsika, khala tcheru!+

  • Yeremiya 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Mawu a Yeremiya+ mwana wa Hilikiya,* mmodzi wa ansembe a ku Anatoti,+ m’dera la Benjamini.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena