Yoswa 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Atachita maere, maerewo anagwera mabanja a Akohati.+ Choncho mizinda 13 inakhala ya ana a wansembe Aroni, omwe anali Alevi. Mizinda yake inachokera m’mafuko a Yuda,+ Simiyoni,+ ndi Benjamini.+
4 Atachita maere, maerewo anagwera mabanja a Akohati.+ Choncho mizinda 13 inakhala ya ana a wansembe Aroni, omwe anali Alevi. Mizinda yake inachokera m’mafuko a Yuda,+ Simiyoni,+ ndi Benjamini.+