Yoswa 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+ 1 Mbiri 6:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Mabanja ena a ana a Kohati anapatsidwa mizinda m’dera lawo kuchokera ku fuko la Efuraimu.+
5 Malire a kum’mawa a cholowa cha ana a Efuraimu potsata mabanja awo, anali Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda,+