Numeri 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Mukapatse Alevi mizinda 6 yoti munthu amene wapha mnzake azikathawirako.+ Kuwonjezera pa mizindayi, mukapatse Aleviwo mizinda ina 42.
6 “Mukapatse Alevi mizinda 6 yoti munthu amene wapha mnzake azikathawirako.+ Kuwonjezera pa mizindayi, mukapatse Aleviwo mizinda ina 42.