Numeri 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yorodano,+ ndiponso mukapereke mizinda itatu tsidya linalo, m’dziko la Kanani.+ Imeneyi ikakhala mizinda yothawirako.
14 Mupereke mizinda itatu tsidya lino la Yorodano,+ ndiponso mukapereke mizinda itatu tsidya linalo, m’dziko la Kanani.+ Imeneyi ikakhala mizinda yothawirako.