Deuteronomo 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Pa nthawi imeneyo, Mose anapatula mizinda itatu kuchigawo chotulukira dzuwa cha Yorodano,+ Deuteronomo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 chifukwa chakuti mwasunga malamulo onsewa amene ndikukupatsani lero mwa kuwatsatira, kuti muzikonda Yehova Mulungu wanu ndi kuyenda m’njira zake nthawi zonse,+ pamenepo mudzawonjezere mizinda inanso itatu pa mizinda imeneyi,+
9 chifukwa chakuti mwasunga malamulo onsewa amene ndikukupatsani lero mwa kuwatsatira, kuti muzikonda Yehova Mulungu wanu ndi kuyenda m’njira zake nthawi zonse,+ pamenepo mudzawonjezere mizinda inanso itatu pa mizinda imeneyi,+