Deuteronomo 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Mukasungadi malamulo onsewa+ amene ndikukupatsani, kukonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda m’njira zake zonse+ ndi kum’mamatira,+ Deuteronomo 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Muzichita mosamala mawu onse amene ndikukuuzani.+ Musawonjezepo kapena kuchotsapo kalikonse.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
22 “Mukasungadi malamulo onsewa+ amene ndikukupatsani, kukonda Yehova Mulungu wanu,+ kuyenda m’njira zake zonse+ ndi kum’mamatira,+
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+