Numeri 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Mose anawauza kuti: “Muchitedi zimenezo. Mutenge zida n’kukonzekera kukamenya nkhondo pamaso pa Yehova.+ Deuteronomo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chotero ndinakulamulani pa nthawi imeneyo kuti, ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna nonse olimba mtima muwoloke, mukuyenda patsogolo pa abale anu, ana a Isiraeli, muli okonzeka ndi zida.+
20 Pamenepo Mose anawauza kuti: “Muchitedi zimenezo. Mutenge zida n’kukonzekera kukamenya nkhondo pamaso pa Yehova.+
18 “Chotero ndinakulamulani pa nthawi imeneyo kuti, ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna nonse olimba mtima muwoloke, mukuyenda patsogolo pa abale anu, ana a Isiraeli, muli okonzeka ndi zida.+