Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Chotero ndinakulamulani pa nthawi imeneyo kuti, ‘Yehova Mulungu wanu wakupatsani dzikoli kuti mulitenge kukhala lanu. Amuna nonse olimba mtima muwoloke, mukuyenda patsogolo pa abale anu, ana a Isiraeli, muli okonzeka ndi zida.+

  • Yoswa 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Akazi anu ndi ana anu aang’ono atsale limodzi ndi ziweto zanu m’dziko lino limene Mose anakupatsani, tsidya lino la Yorodano.+ Koma amunanu, mudzawoloka patsogolo pa abale anu, mutafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+ Inuyo, amuna nonse amphamvu ndi olimba mtima,+ muwoloke kuti mukawathandize abale anu.

  • Yoswa 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Amuna onyamula zida okwanira pafupifupi 40,000, anawoloka pamaso pa Yehova kukamenya nkhondo m’chipululu cha Yeriko.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena