Numeri 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Mose anawauza kuti: “Muchitedi zimenezo. Mutenge zida n’kukonzekera kukamenya nkhondo pamaso pa Yehova.+ Yoswa 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 n’kuwauza kuti: “Inu mwasunga zonse zimene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani,+ ndiponso mwamvera mawu anga m’zonse zimene ndakulamulirani.+
20 Pamenepo Mose anawauza kuti: “Muchitedi zimenezo. Mutenge zida n’kukonzekera kukamenya nkhondo pamaso pa Yehova.+
2 n’kuwauza kuti: “Inu mwasunga zonse zimene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani,+ ndiponso mwamvera mawu anga m’zonse zimene ndakulamulirani.+