Oweruza 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho amuna osankhidwa mwapadera a Isiraeli yense, okwana 10,000 anayandikira mzinda wa Gibeya, ndipo panaulika chinkhondo choopsa. Ana a Benjamini sanadziwe kuti tsoka+ latsala pang’ono kuwagwera. Miyambo 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu amene sadziwa zinthu amakhulupirira mawu alionse,+ koma wochenjera amaganizira za mmene akuyendera.+
34 Choncho amuna osankhidwa mwapadera a Isiraeli yense, okwana 10,000 anayandikira mzinda wa Gibeya, ndipo panaulika chinkhondo choopsa. Ana a Benjamini sanadziwe kuti tsoka+ latsala pang’ono kuwagwera.
15 Munthu amene sadziwa zinthu amakhulupirira mawu alionse,+ koma wochenjera amaganizira za mmene akuyendera.+