Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano mfumu ya Ai itangoona zimenezo, amuna a mumzindawo anakonzekera msangamsanga. M’mawa mwake analawirira kuti akamenyane ndi Aisiraeli. Mfumuyo limodzi ndi anthu ake onse, ananyamuka pa nthawi imene anapangana, ndipo analowera kuchigwa cha m’chipululu. Koma mfumuyo sinadziwe kuti asilikali ena anali atabisala kumbuyo kwa mzindawo.+

  • Oweruza 20:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Pamenepo amuna a Isiraeli anatembenuka,+ ndipo ana a Benjamini anasokonezeka+ chifukwa anaona kuti tsoka lawagwera.+

  • Miyambo 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Njira ya oipa ili ngati mdima.+ Iwo sadziwa chimene chimawapunthwitsa.+

  • Miyambo 28:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Wodala ndi munthu amene amaopa Mulungu nthawi zonse,+ koma woumitsa mtima wake adzagwera m’tsoka.+

  • Miyambo 29:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena