Oweruza 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho amuna osankhidwa mwapadera a Isiraeli yense, okwana 10,000 anayandikira mzinda wa Gibeya, ndipo panaulika chinkhondo choopsa. Ana a Benjamini sanadziwe kuti tsoka+ latsala pang’ono kuwagwera.
34 Choncho amuna osankhidwa mwapadera a Isiraeli yense, okwana 10,000 anayandikira mzinda wa Gibeya, ndipo panaulika chinkhondo choopsa. Ana a Benjamini sanadziwe kuti tsoka+ latsala pang’ono kuwagwera.