Ekisodo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndikunenetsa kuti, ndidzakuchotsani mu nsautso+ ya Aiguputo ndi kukulowetsani m’dziko la Akanani, Ahiti, Aamori,+ Aperizi, Ahivi, ndi Ayebusi,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi.”’+ Ekisodo 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti mngelo wanga adzakutsogolera ndi kukulowetsa m’dziko la Aamori, Ahiti, Aperezi, Akanani, Ahivi ndi Ayebusi, ndipo ndidzawafafaniza ndithu.+
17 Ndikunenetsa kuti, ndidzakuchotsani mu nsautso+ ya Aiguputo ndi kukulowetsani m’dziko la Akanani, Ahiti, Aamori,+ Aperizi, Ahivi, ndi Ayebusi,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi.”’+
23 Pakuti mngelo wanga adzakutsogolera ndi kukulowetsa m’dziko la Aamori, Ahiti, Aperezi, Akanani, Ahivi ndi Ayebusi, ndipo ndidzawafafaniza ndithu.+