-
Yoswa 10:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho mafumu asanu a Aamoriwo+ anakumana pamodzi n’kunyamuka. Mafumuwo anali: Mfumu ya ku Yerusalemu, mfumu ya ku Heburoni, mfumu ya ku Yarimuti, mfumu ya ku Lakisi, ndi mfumu ya ku Egiloni. Mafumu amenewa, pamodzi ndi magulu awo ankhondo anakamanga msasa pafupi ndi mzinda wa Gibeoni, n’cholinga chouthira nkhondo.
-