Yoswa 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Apa m’pamene Horamu mfumu ya ku Gezeri+ anapita kukathandiza mzinda wa Lakisi. Koma Yoswa anapha Horamu ndi anthu ake onse, moti sipanatsale wopulumuka.+
33 Apa m’pamene Horamu mfumu ya ku Gezeri+ anapita kukathandiza mzinda wa Lakisi. Koma Yoswa anapha Horamu ndi anthu ake onse, moti sipanatsale wopulumuka.+