Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 12:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mfumu ya Egiloni,+ imodzi. Mfumu ya Gezeri,+ imodzi.

  • Yoswa 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+

  • Yoswa 21:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Motero anawapatsa mzinda wothawirako+ munthu amene wapha mnzake,+ wa Sekemu,+ ndi malo ake odyetserako ziweto+ m’dera lamapiri la Efuraimu. Anawapatsanso Gezeri+ ndi malo ake odyetserako ziweto,

  • Oweruza 1:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Fuko la Efuraimu nalonso silinapitikitse Akanani amene anali kukhala ku Gezeri, moti Akananiwo anakhalabe pakati pawo ku Gezeriko.+

  • 1 Mafumu 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 (M’mbuyomo, Farao mfumu ya Iguputo inabwera n’kulanda mzinda wa Gezeri n’kuutentha ndi moto. Akanani+ okhala mumzindawo inawapha. Kenako inaupereka kwa mwana wake wamkazi+ monga mphatso pamene anali kukwatiwa ndi Solomo.)

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena