Numeri 35:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kwa ana a Isiraeli, kwa mlendo,+ ndi kwa munthu amene wakhaliratu pakati pawo, mizinda 6 imeneyi ikakhala kothawirako aliyense amene wapha munthu mwangozi.+ Yoswa 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mizindayo ntchito yake ikhale yoti wopha munthu+ mwangozi azithawirako pothawa wobwezera magazi.+
15 Kwa ana a Isiraeli, kwa mlendo,+ ndi kwa munthu amene wakhaliratu pakati pawo, mizinda 6 imeneyi ikakhala kothawirako aliyense amene wapha munthu mwangozi.+