Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake. Ekisodo 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ngati wina wamwalira, pamenepo uzipereka moyo kulipira moyo.+ Numeri 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 wobwezera magazi+ n’kumupeza kunja kwa malire a mzinda wothawirako, n’kumupha, wobwezera magaziyo alibe mlandu wa magazi.
6 Aliyense wokhetsa magazi a munthu, nayenso magazi ake adzakhetsedwa ndi munthu,+ chifukwa Mulungu anapanga munthu m’chifaniziro chake.
27 wobwezera magazi+ n’kumupeza kunja kwa malire a mzinda wothawirako, n’kumupha, wobwezera magaziyo alibe mlandu wa magazi.