Yoswa 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo anatseguladi phangalo n’kumutulutsira mafumu asanuwo: Mfumu ya ku Yerusalemu,+ mfumu ya ku Heburoni,+ mfumu ya ku Yarimuti,+ mfumu ya ku Lakisi ndi mfumu ya ku Egiloni.+
23 Iwo anatseguladi phangalo n’kumutulutsira mafumu asanuwo: Mfumu ya ku Yerusalemu,+ mfumu ya ku Heburoni,+ mfumu ya ku Yarimuti,+ mfumu ya ku Lakisi ndi mfumu ya ku Egiloni.+