Genesis 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho malire a dziko la Akanani anachokera ku Sidoni mpaka ku Gerari+ kufupi ndi Gaza,+ n’kukafika ku Sodomu ndi Gomora+ mpakanso ku Adima+ ndi Zeboyimu,+ kufupi ndi Lasa. Yoswa 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anapitirira mpaka ku Eburoni, Rehobu, Hamoni, Kana, mpaka kumzinda wa anthu ambiri wa Sidoni.+
19 Choncho malire a dziko la Akanani anachokera ku Sidoni mpaka ku Gerari+ kufupi ndi Gaza,+ n’kukafika ku Sodomu ndi Gomora+ mpakanso ku Adima+ ndi Zeboyimu,+ kufupi ndi Lasa.