Levitiko 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu aliyense woperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+ Yoswa 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana a Isiraeli anafunkha katundu yense wa m’mizindayi ndi ziweto zomwe.+ Koma anthu anawapha ndi lupanga kufikira atawamaliza onse.+ Sanasiye munthu aliyense wamoyo.+
29 Munthu aliyense woperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+
14 Ana a Isiraeli anafunkha katundu yense wa m’mizindayi ndi ziweto zomwe.+ Koma anthu anawapha ndi lupanga kufikira atawamaliza onse.+ Sanasiye munthu aliyense wamoyo.+