Ekisodo 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Samalani kuti musachite pangano ndi anthu a m’dziko limene mukupitako+ kuopera kuti ungakhale msampha pakati panu.+ Deuteronomo 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova Mulungu wako adzawapereka ndithu kwa iwe ndipo udzawagonjetse.+ Udzawawononge ndithu+ ndipo usadzachite nawo pangano kapena kuwakomera mtima.+
12 Samalani kuti musachite pangano ndi anthu a m’dziko limene mukupitako+ kuopera kuti ungakhale msampha pakati panu.+
2 Yehova Mulungu wako adzawapereka ndithu kwa iwe ndipo udzawagonjetse.+ Udzawawononge ndithu+ ndipo usadzachite nawo pangano kapena kuwakomera mtima.+