16 Mizinda yokhayi ya anthu awa a mitundu ina imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, ndi imene simuyenera kusiyamo chilichonse chopuma chili chamoyo,+
14 Ana a Isiraeli anafunkha katundu yense wa m’mizindayi ndi ziweto zomwe.+ Koma anthu anawapha ndi lupanga kufikira atawamaliza onse.+ Sanasiye munthu aliyense wamoyo.+