Yoswa 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero, anyamata amene anakazonda dziko aja, anapita kukatulutsa Rahabi, bambo ake, mayi ake, alongo ake, ndi onse amene anali naye. Anatulutsa achibale ake onse,+ ndipo anawapatsa malo kunja kwa msasa wa Isiraeli.
23 Chotero, anyamata amene anakazonda dziko aja, anapita kukatulutsa Rahabi, bambo ake, mayi ake, alongo ake, ndi onse amene anali naye. Anatulutsa achibale ake onse,+ ndipo anawapatsa malo kunja kwa msasa wa Isiraeli.