Yoswa 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musadzaphe bambo anga,+ mayi anga, abale anga ndi alongo anga, limodzi ndi mabanja awo. Mudzatisiye amoyo.”+ Yoswa 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tikubwera ndithu m’dziko muno! Chingwe chofiira ichi uchimangirire pawindo limene watitulutsirapo. Bambo ako ndi mayi ako, abale ako ndi alongo ako, ndi onse a m’nyumba ya bambo ako, uwasonkhanitse kuti adzakhale m’nyumba mwako.+
13 Musadzaphe bambo anga,+ mayi anga, abale anga ndi alongo anga, limodzi ndi mabanja awo. Mudzatisiye amoyo.”+
18 Tikubwera ndithu m’dziko muno! Chingwe chofiira ichi uchimangirire pawindo limene watitulutsirapo. Bambo ako ndi mayi ako, abale ako ndi alongo ako, ndi onse a m’nyumba ya bambo ako, uwasonkhanitse kuti adzakhale m’nyumba mwako.+