-
Esitere 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndingapirire bwanji pamene ndikuona tsoka likugwera anthu a mtundu wanga? Ndipo ndingapirire bwanji pamene ndikuona abale anga akuwonongedwa?”
-