3 Pamenepo Adoni-zedeki mfumu ya Yerusalemu+ anatumiza uthenga kwa Hohamu mfumu ya ku Heburoni,+ kwa Piramu mfumu ya ku Yarimuti,+ kwa Yafiya mfumu ya ku Lakisi+ ndi kwa Debiri mfumu ya ku Egiloni.+ Anatumiza uthenga wakuti:
14 Choncho Hezekiya mfumu ya Yuda anatumiza uthenga kwa mfumu ya Asuri ku Lakisi, wakuti: “Ndachimwa. Siyani kundiukira. Ndikupatsani chilichonse chimene mungandilamule.”+ Chotero mfumu ya Asuri inalamula Hezekiya mfumu ya Yuda kuti apereke matalente* 300 a siliva+ ndi matalente 30 a golide.