Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ansembe aja ataliza malipenga awo,+ asilikaliwo anafuula. Atangomva kulira kwa malipenga, anayamba kufuula mwamphamvu mfuu yankhondo, ndipo mpanda wa mzindawo unayamba kugwa mpaka pansi.+ Zitatero, iwo analowa mumzindawo. Aliyense anathamangira kumeneko, ndi kulanda mzindawo.

  • Yoswa 6:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndiyeno pa nthawiyo, Yoswa analumbira kuti: “Adzakhale wotembereredwa pamaso pa Yehova munthu amene adzamangenso mzinda wa Yerikowu. Akadzangoyala maziko ake, mwana wake woyamba adzafe, ndipo akadzaika zitseko zake za pachipata, mwana wake wotsiriza adzafe.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena